Luka 9:25 - Buku Lopatulika25 Pakuti munthu apindulanji, akadzilemezera dziko lonse lapansi nadzitayapo, kapena kulipapo moyo wake? Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201425 Pakuti munthu apindulanji, akadzilemezera dziko lonse lapansi nadzitayapo, kapena kulipapo moyo wake? Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa25 Nanga ndiye kuti munthu wapindulanji atapata zonse zapansipano, iyeyo nkutaya moyo wake kapena kuuwononga? Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero25 Kodi chabwino ndi chiti kwa munthu, kupata zonse zapansi pano, koma ndi kutaya moyo wake kapena kudziwononga iye mwini? Onani mutuwo |