Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti
- Zotsatsa -




Luka 9:24 - Buku Lopatulika

24 Pakuti aliyense amene akafuna kupulumutsa moyo wake, iye adzautaya; koma aliyense amene akataya moyo wake chifukwa cha Ine, iye adzaupulumutsa uwu.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

24 Pakuti amene aliyense akafuna kupulumutsa moyo wake, iye adzautaya; koma amene aliyense akataya moyo wake chifukwa cha Ine, iye adzaupulumutsa uwu.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

24 Chifukwa wofuna kupulumutsa moyo wake adzautaya, koma wotaya moyo wake chifukwa cha Ine, adzaupulumutsa.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

24 Popeza aliyense amene akufuna kupulumutsa moyo wake adzawutaya, koma aliyense amene adzataya moyo wake chifukwa cha Ine adzawupulumutsa.

Onani mutuwo Koperani




Luka 9:24
8 Mawu Ofanana  

mphindi yakufunafuna ndi mphindi yakumwazika; mphindi yakusunga ndi mphindi yakutaya;


Iye amene apeza moyo wake, adzautaya; ndi iye amene ataya moyo wake, chifukwa cha Ine, adzaupeza.


Iye aliyense akafuna kusunga moyo wake adzautaya, koma iye aliyense akautaya, adzausunga.


Iye wokonda moyo wake adzautaya; ndipo wodana ndi moyo wake m'dziko lino lapansi adzausungira kumoyo wosatha.


Akazi analandira akufa ao mwa kuuka kwa akufa; ndipo ena anakwapulidwa, osalola kuomboledwa,


Ndipo iwo anampambana iye chifukwa cha mwazi wa Mwanawankhosa, ndi chifukwa cha mau a umboni wao; ndipo sanakonde moyo wao kungakhale kufikira imfa.


Usaope zimene uti udzamve kuwawa; taona, mdierekezi adzaponya ena a inu m'nyumba yandende, kuti mukayesedwe; ndipo mudzakhala nacho chisautso masiku khumi. Khala wokhulupirika kufikira imfa, ndipo ndidzakupatsa iwe korona wa moyo.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa