Luka 8:9 - Buku Lopatulika9 Ndipo ophunzira ake anamfunsa Iye, kuti, Fanizo ili lili lotani? Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20149 Ndipo ophunzira ake anamfunsa Iye, kuti, Fanizo ili lili lotani? Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa9 Ophunzira a Yesu adamufunsa za tanthauzo la fanizoli. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero9 Ophunzira ake anamufunsa tanthauzo lake la fanizolo. Onani mutuwo |