Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti
- Zotsatsa -




Luka 8:7 - Buku Lopatulika

7 Ndipo zina zinagwa pakati pa minga; ndi mingayo inaphuka pamodzi nazo, nkuzitsamwitsa.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

7 Ndipo zina zinagwa pakati pa minga; ndi mingayo inaphuka pamodzi nazo, nizitsamwitsa.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

7 Mbeu zina zidagwera pa zitsamba zaminga. Zitsambazo pokula zidalanda chakudya cha mbeu zija.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

7 Mbewu zina zinagwera pakati pa minga, zinakulira pamodzi ndi mingazo ndipo zinalepheretsa mmerawo kukula.

Onani mutuwo Koperani




Luka 8:7
11 Mawu Ofanana  

minga ndi mitula idzakubalira iwe; ndipo udzadya therere la m'thengo:


Pakuti Yehova atero kwa anthu a Yuda ndi kwa Yerusalemu, Limani masala anu, musabzale paminga.


Ndipo iye amene afesedwa kuminga, uyu ndiye wakumva mau; ndipo kulabadira kwa dziko lapansi, ndi chinyengo cha chuma chitsamwitsa mau, ndipo akhala wopanda chipatso.


Koma zina zinagwa paminga, ndipo mingayo inayanga, nkuzitsamwitsa izo.


Ndipo zina zinagwa paminga, ndipo minga inakula, nkuzitsamwitsa, ndipo sizinabale zipatso.


Koma mudziyang'anire nokha, kuti kapena mitima yanu ingalemetsedwe ndi madyaidya ndi kuledzera, ndi zosamalira za moyo uno, ndi kuti tsiku ilo lingafikire inu modzidzimutsa ngati msampha;


Ndipo zija zinagwa kumingazi, ndiwo amene adamva, ndipo m'kupita kwao atsamwitsidwa ndi nkhawa, ndi chuma, ndi zokondweretsa za moyo, ndipo sakhwimitsa zipatso zamphumphu.


Ndipo zina zinagwa pathanthwe; ndipo pakumera zinatofa msanga, chifukwa zinalibe mnyontho.


Ndipo zina zinagwa pa nthaka yokoma, ndipo zinamera, ndi kupatsa zipatso zamakumikhumi. Pakunena Iye izi anafuula, Iye amene ali ndi makutu akumva amve.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa