Luka 8:6 - Buku Lopatulika6 Ndipo zina zinagwa pathanthwe; ndipo pakumera zinatofa msanga, chifukwa zinalibe mnyontho. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20146 Ndipo zina zinagwa pathanthwe; ndipo pakumera zinatofa msanga, chifukwa zinalibe mnyontho. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa6 Mbeu zina zidagwera pa nthaka yapathanthwe. Zidamera, koma nkufota, chifukwa zidaasoŵa chinyontho. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero6 Zina zinagwa pa thanthwe, ndipo pamene zinamera, zinafota chifukwa panalibe chinyezi. Onani mutuwo |