Luka 8:54 - Buku Lopatulika54 Ndipo Iye anamgwira dzanja lake, naitana, nati, Buthu, tauka. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201454 Ndipo Iye anamgwira dzanja lake, naitana, nati, Buthu, tauka. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa54 Yesu adagwira mwanayo pa dzanja nanena mokweza mau kuti, “Mwana iwe, dzuka!” Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero54 Koma Iye anamugwira dzanja lake ndipo anati, “Mwana wanga, dzuka!” Onani mutuwo |