Luka 8:55 - Buku Lopatulika55 Ndipo mzimu wake unabwera, ndipo anauka pomwepo; ndipo Iye anawauza kuti ampatse kanthu ka kudya. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201455 Ndipo mzimu wake unabwera, ndipo anauka pomwepo; ndipo Iye anawauza kuti ampatse kanthu ka kudya. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa55 Pomwepo moyo wake udabwereramo, iyeyo nkudzukadi nthaŵi yomweyo. Kenaka Yesu adaŵauza kuti ampatse chakudya mtsikanayo. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero55 Mzimu wake unabwerera, ndipo nthawi yomweyo anayimirira. Kenaka Yesu anawawuza kuti amupatse chakudya. Onani mutuwo |