Luka 8:20 - Buku Lopatulika20 Ndipo anamuuza Iye, kuti, Amai wanu ndi abale anu alinkuima kunja, nafuna kuona Inu. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201420 Ndipo anamuuza Iye, kuti, Amai wanu ndi abale anu alinkuima kunja, nafuna kuona Inu. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa20 Tsono munthu wina adauza Yesu kuti, “Amai anu ndi abale anu ali panjapa, akufuna kukuwonani.” Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero20 Wina anamuwuza Iye kuti, “Amayi ndi abale anu ayima kunja, akufuna kukuonani.” Onani mutuwo |