Luka 8:21 - Buku Lopatulika21 Koma Iye anayankha, nati kwa iwo, Amai wanga ndi abale anga ndiwo amene akumva mau a Mulungu, nawachita. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201421 Koma Iye anayankha, nati kwa iwo, Amai wanga ndi abale anga ndiwo amene akumva mau a Mulungu, nawachita. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa21 Koma Yesu adati, “Inetu amai anga ndi abale anga ndi anthu amene amamva mau a Mulungu, nkumachitadi zimene mauwo akunena.” Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero21 Yesu anayankha kuti, “Amayi ndi abale anga ndi amene amamva mawu a Mulungu ndi kumachita zimene mawuwo akunena.” Onani mutuwo |