Luka 8:19 - Buku Lopatulika19 Ndipo anadza kwa Iye amake ndi abale ake, ndipo sanakhoze kumfika, chifukwa cha khamu la anthu. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201419 Ndipo anadza kwa Iye amake ndi abale ake, ndipo sanakhoze kumfika, chifukwa cha khamu la anthu. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa19 Amai ake ndi abale ake a Yesu adabwera kunyumbako, koma chifukwa cha kuchuluka kwa anthu, adaalephera kufika pamene panali Iyepo. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero19 Tsopano amayi ndi abale a Yesu anabwera kudzamuona Iye, koma analephera kuti afike pafupi ndi Iye chifukwa cha gulu la anthu. Onani mutuwo |