Luka 7:49 - Buku Lopatulika49 Ndipo iwo akuseama naye pachakudya anayamba kunena mwa okha, Uyu ndani amene akhululukiranso machimo? Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201449 Ndipo iwo akuseama naye pachakudya anayamba kunena mwa okha, Uyu ndani amene akhululukiranso machimo? Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa49 Apo amene ankadya naye adayamba kudzifunsa mumtima mwao kuti, “Kodi ndani uyu wokhululukira ndi machimo omweyu?” Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero49 Alendo enawo anayamba kumanena mʼmitima mwawo kuti, “Uyu ndi ndani amene akhululukiranso machimo?” Onani mutuwo |