Luka 7:45 - Buku Lopatulika45 Sunandipatsa mpsompsono wa chibwenzi; koma uyu sanaleke kupsompsonetsa mapazi anga, chilowere muno Ine. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201445 Sunandipatsa mpsompsono wa chibwenzi; koma uyu sanaleke kupsompsonetsa mapazi anga, chilowere muno Ine. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa45 Iwe sudandimpsomphsone, koma iyeyu chiloŵere changa muno, wakhalira kumpsompsona mapazi anga osalekeza. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero45 Iwe sunandipsompsone, koma mayiyu, kuyambira pamene Ine ndalowa, sanaleke kupsompsona mapazi anga. Onani mutuwo |