Luka 7:4 - Buku Lopatulika4 Ndipo iwo, pakufika kwa Yesu, anampempha Iye koumirira, nati, Ayenera iye kuti mumchitire ichi; Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20144 Ndipo iwo, pakufika kwa Yesu, anampempha Iye koumirira, nati, Ayenera iye kuti mumchitire ichi; Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa4 Pamene adafika kwa Yesu, adampempha kolimba namuuza kuti, “Ameneyu ngwoyeneradi kuti mumchitire zimenezi, Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero4 Iwo atafika kwa Yesu, anamudandaulira kwambiri, nati, “Munthuyu ayenera kuthandizidwa Onani mutuwo |