Luka 7:36 - Buku Lopatulika36 Ndipo mmodzi wa Afarisi anamuitana Iye kuti akadye naye. Ndipo analowa m'nyumba ya Mfarisi, naseama pachakudya. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201436 Ndipo mmodzi wa Afarisi anamuitana Iye kuti akadye naye. Ndipo analowa m'nyumba ya Mfarisi, naseama pachakudya. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa36 Wina wa m'gulu la Afarisi adaitana Yesu kuti akadye kwao. Yesu adapita nakaloŵa m'nyumba ya Mfarisiyo nkukakhala podyera. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero36 Tsopano mmodzi mwa Afarisi anayitana Yesu kuti akadye naye ku nyumba kwake ndipo anapita nakakhala pa tebulo. Onani mutuwo |