Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti
- Zotsatsa -




Luka 7:32 - Buku Lopatulika

32 Angofanana ndi ana akukhala pamsika, ndi kuitanizana wina ndi mnzake, ndi kunena, Ife tinakulizirani chitoliro, ndipo inu simunavine ai; tinabuma maliro, ndimo simunalire ai.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

32 Angofanana ndi ana akukhala pamsika, ndi kuitanizana wina ndi mnzake, ndi kunena, Ife tinakulizirani chitoliro, ndipo inu simunavina ai; tinabuma maliro, ndimo simunalira ai.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

32 Ali ngati ana okangana pa msika, ena akufunsa anzao kuti, “ ‘Tidaakuimbirani ng'oma yaukwati, bwanji inu osavina? Tidaabuma maliro, bwanji inu osalira?’

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

32 Ali ngati ana amene akukangana pa msika, ena akufunsa anzawo kuti, “ ‘Ife tinakuyimbirani chitoliro, koma inu simunavine. Tinakuyimbirani nyimbo zamaliro, koma inu simunalire.’

Onani mutuwo Koperani




Luka 7:32
9 Mawu Ofanana  

Kodi bwanji mtengo wogulira nzeru uli m'dzanja la chitsiru, popeza wopusa alibe mtima?


Ndi m'miseu ya mzinda mudzakhala ana aamuna ndi aakazi akusewera m'miseu yake.


Ndipo anatuluka dzuwa litakwera, naona ena ataima chabe pabwalo;


Ndipo, ndidzafanizira ndi chiyani anthu a mbadwo uno? Ndipo afanana ndi chiyani?


Pakuti Yohane Mbatizi wafika wosadya mkate ndi wosamwa vinyo; ndipo munena, Ali ndi chiwanda.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa