Luka 7:31 - Buku Lopatulika31 Ndipo, ndidzafanizira ndi chiyani anthu a mbadwo uno? Ndipo afanana ndi chiyani? Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201431 Ndipo, ndidzafanizira ndi chiyani anthu a mbadwo uno? Ndipo afanana ndi chiyani? Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa31 “Kaya anthu amakonoŵa ndingaŵafanizire ndi chiyani? Ali ngati chiyani? Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero31 “Kodi ndingawafanizire chiyani anthu a mʼbado uno? Ali ngati chiyani? Onani mutuwo |