Luka 7:30 - Buku Lopatulika30 Koma Afarisi ndi achilamulo anakaniza uphungu wa Mulungu kwa iwo okha, popeza sanabatizidwe ndi iye. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201430 Koma Afarisi ndi achilamulo anakaniza uphungu wa Mulungu kwa iwo okha, popeza sanabatizidwe ndi iye. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa30 Koma Afarisi ndi akatswiri a Malamulo, pakukana kubatizidwa ndi iye, adakana okha zimene Mulungu adafuna kuŵachitira. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero30 Koma Afarisi ndi akatswiri amalamulo anakana cholinga cha Mulungu kwa iwo okha, chifukwa sanabatizidwe ndi Yohane. Onani mutuwo |