Luka 7:2 - Buku Lopatulika2 Ndipo kapolo wa kenturiyo, wokondedwa naye, anadwala, nafuna kutsirizika. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20142 Ndipo kapolo wa kenturiyo, wokondedwa naye, anadwala, nafuna kutsirizika. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa2 Tsono mkulu wina wa gulu la asilikali achiroma 100 anali ndi wantchito amene ankamukonda kwambiri. Wantchitoyo ankadwala, ndipo anali pafupi kufa. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero2 Kumeneko wantchito wa Kenturiyo, amene amamukhulupirira kwambiri, anadwala ndipo anali pafupi kufa. Onani mutuwo |