Luka 7:1 - Buku Lopatulika1 Pamene Yesu adamaliza mau ake onse m'makutu a anthu, analowa mu Kapernao. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20141 Pamene Yesu adamaliza mau ake onse m'makutu a anthu, analowa m'Kapernao. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa1 Yesu atatsiriza kulankhula zonsezi ndi anthu aja, adapita ku Kapernao. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero1 Yesu atamaliza kunena zonsezi pamaso pa anthu amene ankamvetsera, analowa mu Kaperenawo. Onani mutuwo |