Luka 6:1 - Buku Lopatulika1 Ndipo kunali tsiku la Sabata, Iye analinkupita pakati pa minda ya tirigu; ndipo ophunzira ake analinkubudula ngala za tirigu, nazifikisa m'manja mwao, nadya. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20141 Ndipo kunali tsiku la Sabata, Iye analinkupita pakati pa minda ya tirigu; ndipo ophunzira ake analinkubudula ngala za tirigu, nazifikisa m'manja mwao, nadya. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa1 Pa tsiku lina la Sabata Yesu ankadutsa m'minda ya tirigu. Ophunzira ake ankathyolako ngala za tirigu, namazifikisa ndi manja, nkumadya. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero1 Tsiku lina la Sabata Yesu ankadutsa mʼminda yatirigu, ndipo ophunzira ake anayamba kubudula ngala zatirigu, namazifikisa mʼmanja mwawo ndi kumadya. Onani mutuwo |