Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti
- Zotsatsa -




Luka 5:39 - Buku Lopatulika

39 Ndipo palibe munthu atamwa vinyo wakale afuna watsopano; pakuti anena, Wakale ali wokoma.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

39 Ndipo palibe munthu atamwa vinyo wakale afuna watsopano; pakuti anena, Wakale ali wokoma.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

39 “Ndipo munthu akangolaŵa vinyo wakale, watsopano sangamufune. Pajatu amati, ‘Wakale ndiye vinyo chaiye.’ ”

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

39 Ndipo palibe amene atamwa vinyo wakale amafuna watsopano, pakuti amati, ‘Wakale ndi okoma.’ ”

Onani mutuwo Koperani




Luka 5:39
8 Mawu Ofanana  

Yehova atero, Imani m'njira ndi kuona, funsani za mayendedwe akale, m'menemo muli njira yabwino, muyende m'menemo, ndipo mudzapeza mpumulo wa miyoyo yanu; koma anati, Sitidzayendamo.


Ndipo kwa iye wofuna kupita nawe kumlandu ndi kutenga malaya ako, umlolezenso chofunda chako.


Koma kuyenera kutsanulira vinyo watsopano m'matumba atsopano.


Ndipo kunali tsiku la Sabata, Iye analinkupita pakati pa minda ya tirigu; ndipo ophunzira ake analinkubudula ngala za tirigu, nazifikisa m'manja mwao, nadya.


Ndipo iwo onse adachitidwa umboni mwa chikhulupiriro, sanalandire lonjezanolo,


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa