Luka 5:7 - Buku Lopatulika7 ndipo anakodola anzao a m'ngalawa yinayo, adze awathangate. Ndipo anadza, nadzaza ngalawa zonse ziwiri, motero kuti zinalinkumira. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20147 ndipo anakodola anzao a m'ngalawa yinayo, adze awathangate. Ndipo anadza, nadzaza ngalawa zonse ziwiri, motero kuti zinalinkumira. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa7 Adachita kukodola anzao a m'chombo china chija kuti adzaŵathandize. Iwo adabwera, ndipo adadzaza zombo ziŵiri zonse zija mpaka zinali pafupi kumira. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero7 Choncho anakodola anzawo a bwato linalo kuti abwere ndi kuwathandiza, ndipo anabwera nadzaza mabwato onse awiri mpaka kuyamba kumira. Onani mutuwo |