Luka 5:6 - Buku Lopatulika6 Ndipo pamene anachita ichi, anazinga unyinji waukulu wa nsomba; ndipo makoka ao analinkung'ambika; Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20146 Ndipo pamene anachita ichi, anazinga unyinji waukulu wa nsomba; ndipo makoka ao analinkung'ambika; Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa6 Tsono iwo adaponyadi makoka, napha nsomba zambirimbiri, kotero kuti makokawo ankayamba kung'ambika. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero6 Atachita izi, anagwira nsomba zambiri kotero kuti makhoka awo anayamba kungʼambika. Onani mutuwo |