Luka 5:31 - Buku Lopatulika31 Ndipo Yesu anayankha, nati kwa iwo, Amene ali olimba safuna sing'anga; koma akudwala ndiwo. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201431 Ndipo Yesu anayankha, nati kwa iwo, Amene ali olimba safuna sing'anga; koma akudwala ndiwo. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa31 Yesu adaŵayankha kuti, “Anthu amene ali bwino sasoŵa sing'anga ai, koma amene akudwala. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero31 Yesu anawayankha kuti, “Amene sakudwala safuna singʼanga, koma odwala. Onani mutuwo |