Luka 5:28 - Buku Lopatulika28 Ndipo iye anasiya zonse, nanyamuka, namtsata Iye. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201428 Ndipo iye anasiya zonse, nanyamuka, namtsata Iye. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa28 Iye adanyamuka, nasiya zonse, nkumamutsatadi. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero28 Ndipo Levi anayimirira, nasiya zonse ndi kumutsata Iye. Onani mutuwo |