Luka 5:27 - Buku Lopatulika27 Ndipo zitatha izi Iye anatuluka, naona munthu wamsonkho, dzina lake Levi, alikukhala polandirira msonkho, nati kwa iye, Unditsate Ine. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201427 Ndipo zitatha izi Iye anatuluka, naona munthu wamsonkho, dzina lake Levi, alikukhala polandirira msonkho, nati kwa iye, Unditsate Ine. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa27 Pambuyo pake Yesu adatuluka naona munthu wokhometsa msonkho, dzina lake Levi, ali pa ntchito m'nyumba ya msonkho. Adamuuza kuti, “Iwe, unditsate.” Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero27 Zitatha izi, Yesu anachoka ndipo anaona wolandira msonkho dzina lake Levi atakhala mʼnyumba ya msonkho. Yesu anati kwa iye, “Nditsate Ine.” Onani mutuwo |