Luka 5:26 - Buku Lopatulika26 Ndipo chizizwo chinagwira anthu onse ndipo analemekeza Mulungu; nadzazidwa ndi mantha, nanena kuti, Lero taona zodabwitsa. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201426 Ndipo chizizwo chinagwira anthu onse ndipo analemekeza Mulungu; nadzazidwa ndi mantha, nanena kuti, Lero taona zodabwitsa. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa26 Anthu onse aja adazizwa kwambiri, nayamba kutamanda Mulungu. Adagwidwa ndi mantha nati, “Taona zodabwitsa lero.” Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero26 Aliyense anadabwa ndi kuchita mantha ndipo anayamika Mulungu. Iwo anadabwa kwambiri ndipo anati, “Lero taona zinthu zosayiwalika.” Onani mutuwo |