Luka 5:23 - Buku Lopatulika23 Chapafupi nchiti, kunena, Akhululukidwa kwa iwe machimo ako; kapena kunena, Tauka, nuyende? Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201423 Chapafupi nchiti, kunena, Akhululukidwa kwa iwe machimo ako; kapena kunena, Tauka, nuyende? Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa23 Chapafupi koposa nchiti, kunena kuti, ‘Machimo ako akhululukidwa,’ kapena kunena kuti, ‘Dzuka, yamba kuyenda?’ Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero23 Kodi chapafupi ndi chiti: kunena kuti, ‘Machimo ako akhululukidwa,’ kapena kunena kuti, ‘Nyamuka ndipo yenda?’ ” Onani mutuwo |