Luka 5:1 - Buku Lopatulika1 Ndipo panali, pakumkanikiza khamu la anthu, kudzamva mau a Mulungu, Iye analikuimirira m'mbali mwa nyanja ya Genesarete; Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20141 Ndipo panali, pakumkanikiza khamu la anthu, kudzamva mau a Mulungu, Iye analikuimirira m'mbali mwa nyanja ya Genesarete; Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa1 Tsiku lina Yesu adaaimirira pamphepete pa nyanja ya Genesarete, anthu ambirimbiri nkumamupanikiza kuti amve mau a Mulungu. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero1 Tsiku lina Yesu anayima mʼmbali mwa nyanja ya Genesareti, gulu la anthu litamuzungulira likumvetsera mawu a Mulungu. Onani mutuwo |