Luka 4:44 - Buku Lopatulika44 Ndipo Iye analikulalikira m'masunagoge a ku Yudeya. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201444 Ndipo Iye analikulalikira m'masunagoge a ku Yudeya. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa44 Motero Iye ankalalika m'nyumba zamapemphero za ku Yudeya. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero44 Ndipo Iye anapitirirabe kulalikira mʼmasunagoge a ku Yudeya. Onani mutuwo |