Luka 4:4 - Buku Lopatulika4 Ndipo Yesu anayankha nati kwa iye, Kwalembedwa, kuti, Munthu sadzakhala ndi moyo ndi mkate wokha. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20144 Ndipo Yesu anayankha nati kwa iye, Kwalembedwa, kuti, Munthu sadzakhala ndi moyo ndi mkate wokha. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa4 Koma Yesu adati, “Malembo akuti, ‘Munthu sangakhale moyo ndi chakudya chokha.’ ” Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero4 Yesu anayankha kuti, “Zalembedwa: ‘Munthu sadzakhala ndi moyo ndi chakudya chokha.’ ” Onani mutuwo |