Luka 4:3 - Buku Lopatulika3 Ndipo mdierekezi anati kwa Iye, Ngati muli Mwana wa Mulungu, uzani mwala uwu usanduke mkate. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20143 Ndipo mdierekezi anati kwa Iye, Ngati muli Mwana wa Mulungu, uzani mwala uwu usanduke mkate. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa3 Tsono Satana adamuuza kuti, “Ngati ndinu Mwana wa Mulungu, lamulani mwala uli apawu kuti usanduke chakudya.” Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero3 Mdierekezi anati kwa Iye, “Ngati ndiwe Mwana wa Mulungu, uza mwala uwu kuti usanduke buledi.” Onani mutuwo |