Luka 3:21 - Buku Lopatulika21 Pamene anthu onse anabatizidwa, Yesu nayenso anabatizidwa. Iye anali kupemphera, ndipo kuthambo kunatseguka, Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201421 Pamene anthu onse anabatizidwa, Yesu nayenso anabatizidwa. Iye anali kupemphera, ndipo kuthambo kunatseguka, Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa21 Tsiku lina anthu onse aja atabatizidwa, Yesu nayenso adabatizidwa. Pamene Iye ankapemphera, kuthambo kudatsekuka, Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero21 Pamene anthu onse ankabatizidwa, Yesu anabatizidwanso. Ndipo akupemphera, kumwamba kunatsekuka. Onani mutuwo |