Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti
- Zotsatsa -




Luka 3:20 - Buku Lopatulika

20 anaonjeza pa zonsezi ichinso, kuti anatsekera Yohane m'nyumba yandende.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

20 anaonjeza pa zonsezi ichinso, kuti anatsekera Yohane m'nyumba yandende.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

20 Pambuyo pake, kuwonjezera pa zonsezi, Herode adatsekera Yohaneyo m'ndende.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

20 Herode anawonjezanso choyipa ichi pa zonsezo: Anatsekera Yohane mʼndende.

Onani mutuwo Koperani




Luka 3:20
14 Mawu Ofanana  

Ndiponso Manase anakhetsa mwazi wambiri wosachimwa mpaka anadzaza mu Yerusalemu monsemo, osawerenga kulakwa kwake analakwitsa nako Yuda, ndi kuchita choipa pamaso pa Yehova.


ndiponso chifukwa cha mwazi wosachimwa adaukhetsa; popeza anadzaza Yerusalemu ndi mwazi wosachimwa; ndipo Yehova sanafune kukhululukira.


koma ananyodola mithenga ya Mulungu, napeputsa mau ake, naseka aneneri ake, mpaka ukali wa Yehova unaukira anthu ake, mpaka panalibe cholanditsa.


Koma anakhala osamvera, napandukira Inu, nataya chilamulo chanu m'mbuyo mwao napha aneneri anu akuwachitira umboni, kuwabwezera kwa Inu, nachita zopeputsa zazikulu.


Ndapanda ana anu mwachabe; sanamvere kulanga; lupanga lanu ladya aneneri anu, monga mkango wakuononga.


Ndipo pamene Yesu anamva kuti anampereka Yohane, anamuka kulowa ku Galileya;


Pakuti Yohane sanaikidwe m'ndende.


popeza anatsanulira mwazi wa oyera mtima, ndi wa aneneri, ndipo mudawapatsa mwazi amwe; ayenera iwo.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa