Luka 3:19 - Buku Lopatulika19 Koma Herode mfumu ija, m'mene Yohane anamdzudzula chifukwa cha Herodiasi, mkazi wa mbale wake, ndi cha zinthu zonse zoipa Herode anazichita, Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201419 Koma Herode mfumu ija, m'mene Yohane anamdzudzula chifukwa cha Herodiasi, mkazi wa mbale wake, ndi cha zinthu zonse zoipa Herode anazichita, Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa19 Komanso adadzudzula mfumu Herode chifukwa chokwatira Herodiasi, mkazi wa mbale wake, ndiponso chifukwa cha zoipa zina zambiri zimene ankachita. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero19 Koma pamene Yohane anadzudzula Herode wolamulirayo chifukwa chokwatira Herodia, mkazi wa mʼbale wake, ndi zoyipa zina zonse anazichita, Onani mutuwo |