Luka 24:16 - Buku Lopatulika16 Koma maso ao anagwidwa kuti asamzindikire Iye. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201416 Koma maso ao anagwidwa kuti asamzindikire Iye. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa16 Koma maso ao adaachita chidima, mwakuti sadamzindikire. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero16 koma iwo sanamuzindikire. Onani mutuwo |