Luka 24:17 - Buku Lopatulika17 Ndipo anati kwa iwo, Mau awa ndi otani mulandizanawo poyendayenda? Ndipo anaima ndi nkhope zao zachisoni. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201417 Ndipo anati kwa iwo, Mau awa ndi otani mulandizanawo poyendayenda? Ndipo anaima ndi nkhope zao zachisoni. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa17 Tsono Yesu adaŵafunsa kuti, “Kodi mukunka mukukambirana zotani panjira pano?” Apo iwo adaima, nkhope zao zili zakugwa ndi chisoni, Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero17 Iye anawafunsa kuti, “Kodi mukukambirana zotani mʼnjira muno?” Iwo anayima ndi nkhope zakugwa. Onani mutuwo |