Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti

- Zotsatsa -




Luka 24:15 - Buku Lopatulika

15 Ndipo kunali m'kukambirana kwao ndi kufunsana, Yesu mwini anayandikira, natsagana nao.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

15 Ndipo kunali m'kukambirana kwao ndi kufunsana, Yesu mwini anayandikira, natsagana nao.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

15 Akukambirana choncho nkumafunsana, Yesu mwiniwake adayandikira nkumatsagana nawo.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

15 Pamenepo Yesu mwini wake anabwera ndi kuyenda nawo pamodzi;

Onani mutuwo Koperani




Luka 24:15
6 Mawu Ofanana  

Ndipo iwo anafunsana wina ndi mnzake, nati, Sitinatenge mikate.


Pakuti kumene kuli awiri kapena atatu asonkhanira m'dzina langa, ndili komweko pakati pao.


Ndipo iwowa anakambirana nkhani za izi zonse zidachitika.


Koma maso ao anagwidwa kuti asamzindikire Iye.


Ndipo pakulankhula izi iwowa, Iye anaimirira pakati pao; nanena nao, Mtendere ukhale nanu.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa