Luka 24:1 - Buku Lopatulika1 Koma tsiku loyamba la sabata, mbandakucha, anadza kumanda atatenga zonunkhira adazikonza. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20141 Koma tsiku loyamba la sabata, mbandakucha, anadza kumanda atatenga zonunkhira adazikonza. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa1 M'mamaŵa pa tsiku lotsatira Sabata ya Ayuda, azimai aja adapita ku manda, atatenga zonunkhira zimene adaakakonza. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero1 Pa tsiku loyamba la Sabata, mmamawa kwambiri, amayi anatenga zonunkhira napita ku manda. Onani mutuwo |