Luka 23:9 - Buku Lopatulika9 Ndipo anamfunsa Iye mau ambiri; koma Iye sanamyankhe kanthu. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20149 Ndipo anamfunsa Iye mau ambiri; koma Iye sanamyankhe kanthu. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa9 Herode adamufunsa mafunso ambiri, koma Yesu sadamuyankhe kanthu. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero9 Iye anamufunsa mafunso ambiri, koma Yesu sanayankhe. Onani mutuwo |