Luka 23:10 - Buku Lopatulika10 Ndipo ansembe aakulu ndi alembi anaimirira, namnenera Iye kolimba. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201410 Ndipo ansembe aakulu ndi alembi anaimirira, namnenera Iye kolimba. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa10 Akulu a ansembe ndi aphunzitsi a Malamulo adaimirira pomwepo nkumaneneza Yesu kwambiri. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero10 Akulu a ansembe ndi aphunzitsi amalamulo, anayimirira pamenepo ndi kumuneneza kwambiri. Onani mutuwo |