Luka 23:7 - Buku Lopatulika7 Ndipo m'mene anadziwa kuti ali wa mu ulamuliro wake wa Herode, anamtumiza Iye kwa Herode, amene anali iye mwini ku Yerusalemu masiku awa. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20147 Ndipo m'mene anadziwa kuti ali wa m'ulamuliro wake wa Herode, anamtumiza Iye kwa Herode, amene anali iye mwini ku Yerusalemu masiku awa. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa7 Tsono atamva kuti ngwochokeradi ku dera limene Herode amalamulira, adamtumiza kwa Herodeyo, amene nayenso anali m'Yerusalemu masiku omwewo. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero7 Iye atamva kuti Yesu anali pansi pa ulamuliro wa Herode, anamutumiza kwa Herodeyo, amene pa nthawi imeneyo analinso mu Yerusalemu. Onani mutuwo |