Luka 23:53 - Buku Lopatulika53 Ndipo anautsitsa, naukulunga m'nsalu yabafuta, nauika m'manda osemedwa m'mwala, m'menemo sanaike munthu ndi kale lonse. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201453 Ndipo anautsitsa, naukulunga m'nsalu yabafuta, nauika m'manda osemedwa m'mwala, m'menemo sanaike munthu ndi kale lonse. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa53 Tsono adautsitsa naukulunga m'nsalu yoyera yabafuta, nkuuika m'manda. Mandawo anali asanaikemo munthu wina aliyense. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero53 Ndipo anawutsitsa, nawukulunga nsalu yabafuta nawuyika mʼmanda wosemedwa mʼmwala, amene panalibe wina amene anayikidwamo. Onani mutuwo |