Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti
- Zotsatsa -




Luka 23:52 - Buku Lopatulika

52 yemweyo anapita kwa Pilato napempha mtembo wake wa Yesu.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

52 yemweyo anapita kwa Pilato napempha mtembo wake wa Yesu.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

52 Iyeyu adapita kwa Pilato kukapempha mtembo wa Yesu.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

52 Atapita kwa Pilato, iye anakapempha mtembo wa Yesu.

Onani mutuwo Koperani




Luka 23:52
3 Mawu Ofanana  

(amene sanavomereze kuweruza kwao ndi ntchito yao) wa ku Arimatea, mudzi wa Ayuda, ndiye woyembekezera Ufumu wa Mulungu,


Ndipo anautsitsa, naukulunga m'nsalu yabafuta, nauika m'manda osemedwa m'mwala, m'menemo sanaike munthu ndi kale lonse.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa