Luka 23:23 - Buku Lopatulika23 Koma anakakamiza ndi mau okweza, napempha kuti Iye apachikidwe. Ndipo mau ao anapambana. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201423 Koma anakakamiza ndi mau okweza, napempha kuti Iye apachikidwe. Ndipo mau ao analakika. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa23 Koma iwo adamuumiriza mokweza mau kuti Yesu apachikidwe, kufuula kwao kunkakulirakulira. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero23 Koma ndi mawu ofuwulitsa, analimbikirabe kuti Iye apachikidwe, ndipo kufuwulako kunapitirira. Onani mutuwo |