Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti
- Zotsatsa -




Luka 23:18 - Buku Lopatulika

18 Koma iwo onse pamodzi anafuula, nati, Chotsani munthu uyu, mutimasulire Barabasi;

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

18 Koma iwo onse pamodzi anafuula, nati, Chotsani munthu uyu, mutimasulire Barabasi;

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

18 Koma anthu onse aja adayamba kufuula pamodzi kuti, “Mchotseni ameneyu, mutimasulire Barabasi.”

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

18 Onse pamodzi anafuwula kuti, “Muchotseni munthuyu! Timasulireni Baraba!”

Onani mutuwo Koperani




Luka 23:18
10 Mawu Ofanana  

ndiye munthu anaponyedwa m'ndende chifukwa cha mpanduko m'mzinda ndi cha kupha munthu.


koma Petro anaima kukhomo kunja. Chifukwa chake wophunzira winayo amene anadziwika kwa mkulu wa ansembe, anatuluka nalankhula ndi wapakhomo, nalowetsa Petro.


pakuti unyinji wa anthu unatsata, nufuula, Mchotse iye.


Ndipo adamumva kufikira mau awa; ndipo anakweza mau ao nanena, Achoke padziko lapansi munthu wotere; pakuti sayenera iye kukhala ndi moyo.


Koma inu munakaniza Woyera ndi Wolungamayo, ndipo munapempha kuti munthu wambanda apatsidwe kwa inu,


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa