Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti

- Zotsatsa -




Luka 23:19 - Buku Lopatulika

19 ndiye munthu anaponyedwa m'ndende chifukwa cha mpanduko m'mzinda ndi cha kupha munthu.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

19 ndiye munthu anaponyedwa m'ndende chifukwa cha mpanduko m'mudzi ndi cha kupha munthu.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

19 Barabasi anali atamponya m'ndende chifukwa cha kuyambitsa chipolowe mu mzinda, ndiponso kupha munthu.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

19 (Baraba anaponyedwa mʼndende chifukwa choyambitsa chipolowe mu mzinda ndi kupha).

Onani mutuwo Koperani




Luka 23:19
7 Mawu Ofanana  

Ndipo analipo wina dzina lake Barabasi, womangidwa pamodzi ndi opanduka, amene anapha munthu mumpanduko.


Koma iwo onse pamodzi anafuula, nati, Chotsani munthu uyu, mutimasulire Barabasi;


Ndipo anayamba kumnenera Iye, kuti, Tinapeza munthu uyu alikupandutsa anthu a mtundu wathu, ndi kuwaletsa kupereka msonkho kwa Kaisara, nadzinenera kuti Iye yekha ndiye Khristu mfumu.


Ndipo Pilato analankhulanso nao, nafuna kumasula Yesu;


Koma iwo anapunda kunena kuti, Amautsa anthuwo, naphunzitsa mu Yudeya yense, kuyambira ku Galileya ndi kufikira kuno komwe.


Si ndiwe Mwejipito uja kodi, unachita mipanduko kale lija, ndi kutsogolera ambanda aja zikwi zinai kuchipululu?


Koma inu munakaniza Woyera ndi Wolungamayo, ndipo munapempha kuti munthu wambanda apatsidwe kwa inu,


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa