Luka 23:12 - Buku Lopatulika12 Ndipo Herode ndi Pilato anachitana chibwenzi tsiku lomwelo; pakuti kale anadana. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201412 Ndipo Herode ndi Pilato anachitana chibwenzi tsiku lomwelo; pakuti kale anadana. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa12 Tsiku lomwelo Herode ndi Pilato adayamba kuyanjana, chonsecho kale ankadana. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero12 Tsiku limenelo, Herode ndi Pilato anakhala abwenzi. Zisanachitike izi anali adani. Onani mutuwo |