Luka 22:71 - Buku Lopatulika71 Ndipo iwo anati, Tifuniranjinso mboni? Pakuti ife tokha tinamva m'kamwa mwa Iye mwini. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201471 Ndipo iwo anati, Tifuniranjinso mboni? Pakuti ife tokha tinamva m'kamwa mwa Iye mwini. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa71 Pamenepo iwo aja adati, “Tikufuniranji umboni wina? Tadzimvera tokha mau akeŵa.” Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero71 Pamenepo iwo anati, “Nanga tikufuniranjinso umboni wina? Ife tamva kuchokera pa milomo yake.” Onani mutuwo |