Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti
- Zotsatsa -




Luka 22:60 - Buku Lopatulika

60 Koma Petro anati, Munthu iwe, sindidziwa chimene uchinena. Ndipo pomwepo, iye ali chilankhulire, tambala analira.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

60 Koma Petro anati, Munthu iwe, sindidziwa chimene uchinena. Ndipo pomwepo, iye ali chilankhulire, tambala analira.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

60 Koma Petro adati, “Munthu iwe, sindikuzidziŵa zimene ukunenazi.” Ndipo pompo, akulankhulabe, tambala adalira.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

60 Petro anayankha kuti, “Munthu iwe, sindikudziwa zimene ukunena apa.” Pamene iye ankayankhula, tambala analira.

Onani mutuwo Koperani




Luka 22:60
7 Mawu Ofanana  

Yesu anati kwa iye, Indetu ndinena kwa iwe, kuti usiku uno, tambala asanalire, udzandikana Ine katatu.


Ndipo Iye anati, Ndikuuza iwe, Petro, sadzalira tambala lero lino kufikira udzakana katatu kuti sundidziwa Ine.


Ndipo patapita ngati ora limodzi, wina ananenetsa, kuti, Zoonadi, munthu uyunso anali naye, pakuti ndiye Mgalileya


Ndipo Ambuye anapotoloka, nayang'ana Petro. Ndipo Petro anakumbukira mau a Ambuye, kuti anati kwa iye, Asanalire tambala lero lino, udzandikana Ine katatu.


Pamenepo Petro anakananso; ndipo pomwepo analira tambala.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa